sent_id
stringlengths 3
7
⌀ | english
stringlengths 3
1.06k
| chichewa
stringlengths 4
3.03k
| topic
stringclasses 8
values | source
stringclasses 17
values |
---|---|---|---|---|
en11503 | Sports diplomacy may transcend cultural differences and bring people together. The use of sports and politics has had both positive and negative implications over history | Kukambirana zamasewera kumatha kupitilira kusiyana kwa chikhalidwe ndikubweretsa anthu pamodzi. Kugwiritsa ntchito masewera ndi ndale kwakhala ndi zotsatira zabwino ndi zoipa pa mbiri yonse
| sports | online news |
en11504 | Sports competitions or activities have had the intention to bring about change in certain cases | Mpikisano wamasewera kapena zochitika zakhala ndi cholinga chobweretsa kusintha pazochitika zina
| sports | online news |
en11505 | In the case of Apartheid, sport was used to isolate South Africa and bring about a major overhaul in the country's social structure. While ethnicity, race, social class and more can cause division, sports is also said to help blend differences | Pankhani ya tsankho, masewera adagwiritsidwa ntchito kupatula dziko la South Africa ndikubweretsa kusintha kwakukulu kwa chikhalidwe cha dzikolo. Ngakhale mafuko, mtundu, chikhalidwe cha anthu ndi zina zikhoza kuyambitsa kugawanikana, masewera amatha kutathandiza kugwirizanitsa kusiyanaku.
| sports | online news |
en11506 | Additionally, numerous athletes have sought political office such as Imran Khan and George Weah, some of them unsuccessfully, on either the national level or the sub-national current | Kuphatikiza apo, othamanga ambiri akufunafuna maudindo andale monga Imran Khan ndi George Weah, ena mwa iwo sanachite bwino, mwina pamlingo wadziko lonse kapena wapadziko lonse lapansi.
| sports | online news |
en11507 | Football stadiums in Europe have acted as both places of refuge as well as sites of terrorist attacks and political uprisings | Mabwalo amasewera a mpira ku Europe akhala ngati malo othawirako komanso malo omwe zigawenga zimaukira komanso zipolowe zandale | sports | online news |
en11508 | With a coinciding sharp rise in popularity at a time of high political intensity, football became politicized | Ndikudziwika bwino kwa masewerawa panthawi yazandale, mpira udakhala chida chandale.
| sports | online news |
en11509 | While many clubs don't have a fixed political identity, some clubs are known to have clear leanings; an example is supporters of Sunderland AFC predominantly lean to the political left and often sing "The Red Flag" during games | Ngakhale kuti makalabu ambiri alibe chidziwitso chokhazikika pa ndale, makalabu ena amadziwika kuti ali ndi kutsamila kodziwika; Chitsanzo ndi otsatira a Sunderland AFC omwe amatsamira kumanzere kwa ndale ndipo nthawi zambiri amaimba "Mbendera Yofiira" pamasewera.
| sports | online news |
en11510 | I walked down Seventh Avenue and saw grown men weeping like children, and women sitting in the curbs with their head in their hands. All across the country that night when the news came out that Joe was knocked out, people cried | Ndinayenda mumsewu wa Seventh ndipo ndinaona amuna akuluakulu akulira ngati ana, ndipo akazi atakhala m'mphepete mwa msewu mutu uli m'manja. M'dziko lonselo usiku umenewo pamene nkhani inamveka yoti Joe wagwonjetsedwa, anthu analira
| sports | online news |
en11511 | Schmeling was, however, welcomed home with a jubilant reaction. Hitler sent his wife flowers with the message: "For the wonderful victory of your husband, our greatest German boxer, I must congratulate you with all my heart | Schmeling adalandiridwa kunyumba ndi chisangalalo. Hitler anatumiza maluwa kwa mkazi wake ndi uthenga wakuti: “Pachipambano chodabwitsa cha mwamuna wako, wankhonya wathu wamkulu wa ku Germany, ndiyenera kukuthokoza ndi mtima wanga wonse.
| sports | online news |
en11512 | This thought gave me the strength to succeed in this fight. It gave me the courage and the endurance to win this victory for Germany's colours | Lingaliro limeneli linandipatsa mphamvu kuti ndipambane pankhonta imeneyi. Zinandilimbitsa mtima ndikupilira kuti ndipambanire makaka a dziko la Germany
| sports | online news |
en11513 | Louis later recalled the pressure on him before the fight: "I knew I had to get Schmeling good. I had my own personal reasons and the whole damned country was depending me | Pambuyo pake Louis anakumbukira chiphinjo chomwe anali nacho asanamenyane: "Ndinadziwa kuti ndiyenera kumogonjetsa Schmeling bwino. Ndinali ndi zifukwa zanga zanga ndipo dziko lonse linali likudalira ine.
| sports | online news |
en11514 | After earning the championship, Clay converted his religion to Islam, which instigated conflict with his boxing career. He also abandoned his name that was given to his slave ancestors and adopted Muhammad Ali | Atapambana mpikisanowu, Clay anasitha chipembedzo chake kukhala wachisilamu, zomwe zidayambitsa mikangano ndi ntchito yake ya nkhonya. Adasiyanso dzina lake lomwe adapatsidwa kwa makolo ake akapolo ndikukhala Muhammad Ali
| sports | online news |
en11515 | On April 28, 1967, he refused to serve in the Army during the Vietnam War, stating religious reasons that it goes against the Qur'an's teaching | Mu chaka 1876, mwezi wa April pa 28, iye anakana kulowa usilikali pa nthawi ya nkhondo ya ku Vietnam, ndipo ananena zifukwa zachipembedzo zomwe zimatsutsana ndi chiphunzitso cha Qur'an.
| sports | online news |
en11516 | He then became an icon of not only the civil rights struggle, but also the anti-Vietnam War movement. However, he was convicted of draft evasion, sentenced to five years in prison and stripped of his championship | Kenako adakhala mtsogoleri osati womenyera ufulu wachibadwidwe kokha, komanso gulu lodana ndi nkhondo yak u Vietnam. Komabe, adapezeka wolakwa chifukwa chozemba usilikali, adaweruzidwa kuti akhale m'ndende zaka zisanu ndikulandidwa mphoto zake zonse | sports | online news |
en11517 | It was not until a lawsuit in 1970 that Ali redeemed his title. He would continue in historical boxing matches now known as Rumble in the Jungle in 1974 and Thrilla in Manila in 1975, defeating George Foreman and Joe Frazier, respectively | Kufikira pa mlandu wake mu chaka cha 1970 pamene Ali adatengaso mphoto yake. adapitiliza m'maseŵera ankhonya omwe tsopano amadziwika kuti Rumble in the Jungle mu chaka 1974 ndi Thrilla ku Manila mu chaka cha 1975, kugonjetsa George Foreman ndi Joe Frazier, motsatizana.
| sports | online news |
en11518 | In 2008, the England and Wales Cricket Board cancelled Zimbabwe's 2009 tour of England and suspended all bilateral relations between the two states in response to the situation regarding the 2008 Zimbabwean presidential election | Mu chaka cha 2008, bungwe la Cricket la England ndi Wales linaletsa ulendo woyendera dziko la Zimbabwe mu chaka cha 2009 ndipo linayimitsa mgwirizano wa mayiko awiriwa potengera zomwe zinkachitika pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko mu chaka cha 2008.
| sports | online news |
en11519 | In 2021, Formula One announced that one of its event will be held in Saudi Arabia. The move has been criticized by many human rights group as example of Saudi Arabia "sportswashing" | Mu chaka 2021, Formula One idalengeza kuti gawo limodzi mwazochitika zake zidzachitikira ku Saudi Arabia. Kusinthaku kwadzudzulidwa ndi mabungwe ambiri omenyera ufulu wachibadwidwe ngati chitsanzo chowononga masewera ku Saudi Arabia
| sports | online news |
en11520 | The move received mixed reaction among fans, some fans criticized the move as ironic as some races are still being held in countries with poor human rights record | Kusinthaku kwakhudza otsatira mosiyanasiyana , wotsatira ena adadzudzula izi ngati zodabwitsa chifukwa mpikisano ina ikuchitikabe ku maiko omwe alibe mbiri yabwino yaufulu wachibadwidwe.
| sports | online news |
en11521 | The Olympics were used as a method of hardening the German spirit and instilling unity among German youth | Masewera a Olimpiki amagwiritsidwa ntchito ngati njira yolimbilitsa mtima ndikukhazikitsa umodzi pakati pa achinyamata aku Germany
| sports | online news |
en11522 | It was also believed that sport was a "way to weed out the weak, and other undesirables | Ankakhulupiriranso kuti masewera ndi “njira yochotsera ofooka, ndi zina zosafunika
| sports | online news |
en11523 | The politicization of sports have a quite long history in China. Since the 1970s, China has been using sport to boost its soft power as sporting nations | Ndale pa masewera ndi mbiri yokhazikika ku China. Kuyambira m'ma 1970, dziko la China lakhala likugwiritsa ntchito masewera kuti iwonjezere mphamvu zake ngati mayiko wochitsa masewera.
| sports | online news |
en11524 | A study of elections has shown that the result of sports events can affect the overall results. A study published in the Proceedings of the National Academy of Sciences showed that when the home team wins the game before the election, the incumbent candidates can increase their share of the vote by 1.5 percent, while a loss had the opposite effect | Kafukufuku wa zisankho wasonyeza kuti zotsatira za zochitika zamasewera zikhoza kukhudza zotsatira zonse. Kafukufuku wofalitsidwa mu Proceedings of the National Academy of Sciences anasonyeza kuti gulu la kunyumba likapambana maseŵerawo chisankho chisanachitike, ofuna kusankhidwawo akhoza kuwonjezera mavoti awo ndi 1.5 peresenti, pamene kuluza kukhoza kukhala ndi zotsatira zosiyana.
| sports | online news |
en11525 | Though many believe that sport is apolitical and neutral, sport is intricately enmeshed within the larger socio-political context in which it operates | Ngakhale ambiri amakhulupirira kuti masewera ndi andale komanso osalowererapo, masewerawa amakhudzidwa kwambiri ndi chikhalidwe cha ndale momwe amachitikira.
| sports | online news |
en11526 | Malaysian politicians have used the mass appeal of sports to garner votes, Deol noted. They often promise new stadiums and other sports infrastructure while campaigning | Andale aku Malaysia agwiritsa ntchito chidwi chachikulu chamasewera kuti apeze mavoti, adatero Deol. Nthawi zambiri amalonjeza mabwalo amasewera atsopano ndi zida zina zamasewera pomwe akumemeza anthu
| sports | online news |
en11527 | Some ministers are the patrons or presidents of football associations. In Malaysia, sport is therefore closely linked to formal politics | Nduna zina ndi woyan’ganira kapena atsogoleri a mabungwe ampira. Ku Malaysia, masewera amalumikizana kwambiri ndi ndale
| sports | online news |
en11528 | Looking at sport through a political lens means looking at who has access to sport and who does not. While sport is often regarded as an equalizer, it can only work this way if a conscious effort is made to ensure that all have equal access. Hence, understanding the politics of sport is essential to informing policy on sport access | Kuyang'ana masewera kudzera m'ndondomeko yandale kumatanthauza kuyang'ana omwe ali ndi mwayi wochita masewera ndi omwe alibe. Ngakhale kuti masewera nthawi zambiri amawonedwa ngati olinganitsa, amatha kugwira ntchito motere ngati ntchito yoyesetsa ikuchitika kuti onse akhale ndi mwayi wofanana. Chifukwa chake, kumvetsetsa ndale zamasewera ndikofunikira pakudziwitsa mfundo zamasewera
| sports | online news |
en11529 | Sport can also be used to bring about peace in society. As Deol noted, sport has been the best solution to resolve racial tensions in Malaysia | Masewera atha kugwiritsidwanso ntchito kubweretsa mtendere pakati pa anthu. Monga Deol ananenera, masewera akhala njira yabwino yothetsera mikangano yamitundu ku Malaysia
| sports | online news |
en11530 | He emphasized that instead of focusing only on elite athletes, sport at a grassroots level should be mobilized to become a vehicle for peace. Panelists emphasized, however, that in order for sport to achieve peace, it must be designed in a way to do so | Iye wanenetsa kuti m’malo mongoyang’ana ochita masewera apamwamba okha, masewera a mlingo wa pansi kwambiri akuyenera kukonzedwa kuti akhale njira ya mtendere. Koma akuluakulu aboma atsindika kuti, kuti masewera akhazikitse mtendere, akuyenera kukonzedwa m'njira yoti akwanitse izi. | sports | online news |
en11531 | First, sport provides a stage for public visibility, attention, and awareness. For a politician, virtually all publicity is good. Appearing at an event, whether throwing out the first pitch of a big game or simply sitting in the stands is bound to attract cameras and a mention in the local newspaper | Choyamba, masewera amapereka mwayi ku gulu la anthu, chidwi, ndi kuzindikilitsa. Kwa wandale, pafupifupi kuwonekera kulikonse ndikwabwino. Kuwonekera pamwambo, kaya kupeleka bawlo la masewero poyambirira a masewero aakulu kapena kungokhala ku malo owonelera kumayenera kukopa wojambula ndi kutchulidwa m'nyuzipepala yakomweko.
| sports | online news |
en11532 | At the very minimum, sport provides a safe stage for a politician to remind the public of his/her existence | Pang'ono ndi pang'ono, masewera amapereka malo otetezeka kwa ndale kuti akumbutse anthu zakupezeka kwawo
| sports | online news |
en11533 | Secondly and more significantly, sport can help solidify a politician’s reputation, identity, and social status. It can demonstrate that a politician is, at least on some level, just one of the guys | Kachiwiri komanso kowonjezereka, masewera angathandize kulimbitsa mbiri ya wandale, mbiri yake, komanso chikhalidwe chake. Zitha kuwonetsa kuti wandale ndi, pamlingo wina, m'modzi mwa anthuwo
| sports | online news |
en11534 | When a politician appears at, say, a college netball game, it shows they share a common passion with the wider public. In the same way a political candidate drinking a beer at the local watering hole has become an obligatory photo-op, appearing at a sporting event proves he or she isn’t an elitist snob | Wandale akawonekera, titi, masewera a mpira wa ku sukulu yawukachenjede, zimawonetsa kuti ali ndi chidwi ndi gululo. Momwemonso munthu wandale yemwe amamwa mowa pamalo omwera mowa m'deralo amakhala chithunzi chovomerezeka, kuwonekera pamasewera kumatsimikizira kuti si munthu wamba.
| sports | online news |
en11535 | And much like it is important that the candidate knows how to hold the pint glass in the photo-op at the bar, it is important the politician simply acts like an ordinary sports fan at the game | Ndipo monga kufunikira kuti wosankhidwayo adziwe momwe angagwirile botolo la mowa pazithunzi ku malo omwera mowa, ndikofunikira kuti wandale akhale ngati munthu Wamba wokonda masewerawo
| sports | online news |
en11536 | Of course, sport, like the bar, has a long tradition as masculine space; sometimes it’s even characterized as a “refuge of masculinity.” This provides yet another barrier to women seeking success in the political realm, which itself can be seen as another of the “last refuges | Zoonadi, masewera, monga komwera mowa , ali ndi mwambo wokhazikika kuti ndi malo achimuna; nthawi zina amatchulidwanso ngati "pothawirapo amuna." Izi zimapereka chotchinga chinanso kwa amayi omwe akufuna kuchita bwino pazandale, zomwe zitha kuwonedwa ngati zina mwa "zothawirako pomaliza."
| sports | online news |
en11537 | In any case, the manner in which sport provides the chance to connect with communities that bridge political and ideological divides makes it particularly appealing to those seeking public approval | Mulimonse momwe zingakhalire, momwe masewera amaperekera mwayi wolumikizana ndi madera omwe amayambitsa mikangano yandale ndi yandale zimapangitsa kukhala kosangalatsa kwambiri kwa omwe akufuna kuvomerezedwa ndi anthu.
| sports | online news |
en11538 | This speaks to the third way in which sport is crucial to political leadership. Politicians love to be associated with the fun, positive energy associated with modern sports, not to mention the aura of excellence, excitement, and success | Izi zikukamba za njira yachitatu yomwe masewera ali ofunikira pa utsogoleri wa ndale. Andale amakonda kugwirizana ndi zosangalatsa, mphamvu zabwino zogwirizana ndi masewera amakono, komanso kupambana, chisangalalo, ndi kupambana.
| sports | online news |
en11539 | These appearances work toward the creation of legitimacy, likeability, and credibility through the transference of the positive feelings associated with sports, especially those that are popular and successful | Mawonekedwewa amathandizira kuti pakhale kuvomerezeka, kufunidwa, ndi kudalirika kudzera pagawana malingaliro abwino okhudzana ndi masewera, makamaka omwe ali otchuka komanso opambana.
| sports | online news |
en11540 | Sport provides a public activity that is often as much about the audience as the participants. In doing so, a basis for some sort of common, unified, and collective identity is provided | Masewera amapereka zochitika zapagulu zomwe nthawi zambiri zimakhala zokhudzana ndi wotenga nawo mbali. Pochita izi, maziko amtundu wina wodziwika, wogwirizana, komanso wagulu amaperekedwa
| sports | online news |
en11541 | The president also used the event to craft and convey his unique, post-1960s vision of social justice and racial harmony | Mtsolgoleri wa dziko adagwiritsanso ntchito mwambowu kupanga ndikuwonetsa masomphenya ake apadera, pambuyo pa zaka za m'ma 1960 a chilungamo cha chikhalidwe cha anthu komanso mgwirizano pakati pa mitundu.
| sports | online news |
en11542 | It was a vision that was based upon individual opportunity and a community in which individuals (not groups) were united around a common cause, had equal access to opportunity, and drew heavily if implicitly on the ideals about fair play, competition, hard work, and individual effort that circulate widely within the world of sport itself | Anali masomphenya omwe anali oziwika pa mwayi wa anthu komanso gulu lonse la anthu anali ogwirizana pazifukwa chofuna zofanana, anali ndi mwayi wofanana, ndipo anabwera pamodzi ndi malingaliro okhudza kusewera mwachilungamo, mpikisano, kugwira ntchito mwakhama, ndi kuyesetsa kwamunthu komwe kumafalikira kwambiri mu zamasewera | sports | online news |
en11543 | It was a moving portrait, a stirring vision made all the more powerful by the fact that many who heard it thought of it as nothing more than a story about an all-American event and a set of ideals that any and every American could agree upon | Chinali chithunzi chochititsa chidwi, masomphenya ochititsa chidwi kwambiri chifukwa chakuti ambiri amene anamva nkhaniyi ankaganiza kuti si nkhani chabe ya zochitika za ku America komanso mfundo zimene aliyense wa ku America angagwirizane nazo.
| sports | online news |
en11544 | It does not take a great imagination, only a sociological one, to see that sport is indeed a powerful political platform | Sizitengera kulingalira kwakukulu, kokha kwa chikhalidwe cha anthu, kuwona kuti masewera alidi nsanja yamphamvu yandale.
| sports | online news |
en11545 | Sport is actively sought as a stage on which to be seen and solidify one’s public identity, political legitimacy, and leadership qualities | Masewera amafunidwa kwambiri ngati siteji yomwe angawonekere ndikulimbitsa kudziwika kwake pagulu, kuvomerezeka pazandale, komanso utsogoleri.
| sports | online news |
en11546 | Sport is a powerful and important political force. But it is most powerful when people are least aware of it—when people believe that nothing important or unusual is going on; in other words, when the politics are hidden or masked, seen as natural or organic | Masewera ndi amphamvu komanso wofunika kwambiri pandale. Koma amakhala amphamvu kwambiri pamene anthu sakudziŵa—pamene anthu amakhulupirira kuti palibe chinthu chofunika kapena chachilendo chimene chikuchitika; mwa kuyankhula kwina, pamene ndale zabisika kapena, zikuwoneka ngati ndi m’mene zimakhalira
| sports | online news |
en11547 | For politicians, this means that they must engage in a delicate dance because even as they use sport for a political purpose it is essential that sport retain its status as a somehow sacred or at least special space | Kwa andale, izi zimatanthauza kuti akuyenera kupanga zinthu zawo mosamala chifukwa ngakhale amagwiritsa ntchito masewera pazandale ndikofunikira kuti masewera azikhalabe ngati opatulika kapena malo apadera.
| sports | online news |
en11548 | For the rest of us, trying to be aware of what is going on in order that we might participate in both politics and sports with our eyes open, as equals rather than as dupes subject to the manipulation and exploitation of others | Kwa tonsefe, kuyesera kudziŵa zimene zikuchitika kuti tithe kutenga nawo mbali m’zandale ndi zamasewera ndi maso athu, monga olingana m’malo mwawochitilidwa chinyengo amene ndi kudyeredwa masuku pamutu ndi ena.
| sports | online news |
en11549 | All eyes will be on Lionel Messi, the world's greatest footballer, when he walks out with Barcelona in the Champions League final. If you watch carefully, you may see him crossing himself as he strides onto the pitch | Maso onse adzakhala pa Lionel Messi, wosewera mpira wamkulu padziko lonse lapansi, akakhale akulowa ndi Barcelona pamasewera omaliza a Champions League. mukayang'anitsitsa, mukhoza kumuwona akupanga chizindikiro cha mtamda pamene akulowa pabwalo
| sports | online news |
en11550 | On the opposing side, Manchester United striker Javier Hernandez has been known to pray on the pitch | Kumbali inayo, osewera wa Manchester United Javier Hernandez amadziwika kuti amapemphera pabwalo la mpira
| sports | online news |
en11551 | Messi and Hernandez are not the only footballers to reveal their beliefs during the pursuit of their sport. Real Madrid star Kaka has often talked about his faith, praying on the pitch and thanking God for his rapid recovery from a broken back | Messi ndi Hernandez si osewera okhawo omwe amawonetsa zomwe amakhulupirira panthawi yamasewera awo. Kaka yemwe ali katswiri wa Real Madrid nthawi zambiri amalankhula za chikhulupiriro chake, ampemphera pabwalo la mpira ndikuthokoza Mulungu chifukwa chochira msanga pamsana wothyoka.
| sports | online news |
en11552 | Other sportsmen, from Muhammad Ali to Jonathan Edwards, the triple jumper, have also spoken about the power of faith. They believe in different theologies, but all would assert they have benefited from their convictions. | Osewera ena, kuyambira Muhammad Ali mpaka Jonathan Edwards, wodumpha katatu, akhala akuyakhulanso za mphamvu ya chikhulupiriro. Amakhulupirira ziphunzitso zaumilungu zosiyanasiyana, koma onse akhoza kunena kuti apindula ndi zikhulupiriro zawo.
| sports | online news |
en11553 | As Ali put it in the build-up to his clash with George Foreman in 1974: "How can I lose with Allah on my side?" | Monga Ali adanenera pokonzekera kukumana ndi George Foreman mu chaka cha 1974: "Ndingagonje bwanji pamene Mulungu ali mbali yanga?"
| sports | online news |
en11554 | Atheists will regard the idea that religion can make a difference to outcomes in sport as fanciful. But it is possible to put aside the issue of whether or not God exists and just examine the impact of faith on performance | Osakhulupirira kuti kuli Mulungu amaona lingaliro lakuti chipembedzo chikhoza kupangitsa kusiyana kwa zotsatira zamasewera kukhala chongopeka. Koma ndizotheka kuyiyika pambali nkhani yoti Mulungu alipo kapena ayi ndikungoyang'ana momwe chikhulupiriro chimakhudzira maseweredwe
| sports | online news |
en11555 | I always prepared my game with prayer. I committed all things to God, without worry. These prayers make me calmer and more secure and I forget the fear of losing. It resulted in good play | Nthawi zonse ndimakonzekera masewera anga ndi pemphero. Ndinapereka zinthu zonse kwa Mulungu, popanda nkhawa. Mapempherowa amandipangitsa kukhala wodekha komanso wotetezeka kwambiri ndipo ndimayiwala kuopa kuluza. Zimapangitsa kusewera bwino
| sports | online news |
en11556 | All of which suggests that religious conviction really can boost performance, but only if you truly believe | Zonsezi zikusonyeza kuti kukhudzika kwachipembedzo kumatha kulimbikitsa ntchito, koma ngati mukhulupiriradi
| sports | online news |
en11557 | Many believe that sport transcends politics. But it can also be used as a political tool to distract attention from human rights abuses, making sportspeople and fans complicit | Ambiri amakhulupirira kuti masewera amaposa ndale. Koma atha kugwiritsidwanso ntchito ngati chida chandale chosokoneza chidwi pakuphwanya ufulu wa anthu, kupangitsa osewera ndi wotsatira kukhala ogwirizana.
| sports | online news |
en11558 | This is ‘sportswashing.’ The Qatari government is hoping it can appropriate the positive associations fans have with football to elevate its own status on the international stage and distract from its ongoing human rights violations | Uku ndi 'kutsuka masewera.' Boma la Qatar likuyembekeza kuti litha kutengera mayanjano abwino omwe okonda mpira ali nawo kuti akweze mbiri yake pamasewera apadziko lonse lapansi ndikuchotsa chidwi cha anthu pa kuphwanya kwawo ufulu wachibadwidwe.
| sports | online news |
en11559 | But what’s so bad about a country with a troubling human rights record supporting or hosting an unrelated sporting competition? | Koma ndi chiyani choyipa chokhudza dziko lomwe lili ndi mbiri yovuta yaufulu wachibadwidwe kuthandizira kapena kuchititsa mpikisano wamasewera osagwirizana?
| sports | online news |
en11560 | Does watching or travelling to that country to attend the competition make spectators complicit in human rights abuses? And shouldn’t sport be kept separate from politics? To answer these questions, we first need to be clear about what sportswashing is | Kodi kuonera kapena kupita kudzikolo kukachita nawo mpikisanowu kumapangitsa owonerera kuchita nawo kuphwanya ufulu wa anthu? Ndipo masewera sakuyenera kukhala osiyana ndi ndale? Kuti tiyankhe mafunsowa, choyamba tifunika kumveketsa bwino za kutsuka zamasewera ndi chiyani
| sports | online news |
en11561 | Sportswashing refers to states – sometimes individiuals or corporations – that seek to use sport to bolster their image by distracting from their wrongdoing | Kutsuka pamasewera kumatanthauza mayiko - nthawi zina anthu kapena mabungwe - omwe amafuna kugwiritsa ntchito masewera kuti alimbikitse mawonekedwe awo pochotsa chidwi cha anthu pazolakwitsa zawo.
| sports | online news |
en11562 | It’s typically not just a matter of hosting games or supporting a national team but rather pumping money into sport specifically to change people’s attitudes about them | Nthawi zambiri si nkhani yongochititsa masewera kapena kuthandiza timu ya dziko koma m'malo mwake kupeleka ndalama kumasewera kuti asinthe malingaliro a anthu pa iwo.
| sports | online news |
en11563 | Sport is more than just entertainment. It exemplifies what many people believe to be noble or aspirational virtues: discipline, hard work, individual excellence, teamwork | Masewera si zosangalatsa chabe. Zimapereka chitsanzo cha zomwe anthu ambiri amakhulupirira kuti ndi zabwino kapena zokhumba zabwino: khalidwe, kugwira ntchito molimbika, kuchita bwino payekha, kugwira ntchito limodzi.
| sports | online news |
en11564 | For spectators, sport generates intense feelings of belonging and a shared identity that verges on the sacred; a win for one’s team elevates oneself and one’s whole community. Sport also reaches a wide audience, including people who may not actively follow politics or world affairs | Kwa owonerera, masewerawa amapangitsa kuti anthu azidzimva kuti ndi ofunika kwambiri komanso kuti adzidziwika kuti ndi opatulika; kupambana kwa timu kumakweza munthu ndi gulu lonse. Masewera amafikiranso anthu ambiri, kuphatikiza anthu omwe samatsatira ndale kapena zochitika zapadziko lonse lapansi
| sports | online news |
en11565 | There’s another upshot of sportswashing: given many people have powerful feelings about sport, if the majority of the news they hear about Qatar is connected to their beloved game, then their feelings for sport can bleed over into their impression of the country | Palinso chithunzithunzi china chakutsuka masewera: chifukwa anthu ambiri ali ndi malingaliro amphamvu pamasewera, ngati nkhani zambiri zomwe amamva za Qatar zikugwirizana ndi masewera omwe amawakonda, ndiye kuti malingaliro awo pamasewera amatha kutengera dzikolo. | sports | online news |
en11566 | Once that positive connection with sport is established, it can come to clash with negative associations they have about human rights violations, causing cognitive dissonance, which describes a tension between two opposing ideas | Chiyanjano chabwinocho ndi masewera chikakhazikitsidwa, chimatha kutsutsana ndi mayanjano oyipa omwe amakhala nawo okhudza kuphwanya ufulu wa anthu, zomwe zimayambitsa kusokonezeka kwa chidziwitso, komwe kumafotokoza kusamvana pakati pa maganizo awiri otsutsana.
| sports | online news |
en11567 | Most people tend to dislike the feeling of dissonance and will seek to eliminate it, often by ejecting one of the dissonant thoughts. Sportswashing nations hope that the ejected thought is the one about human rights rather than sport | Anthu ambiri samakonda kukhala osokonezedwa ndipo amafunafuna kuthetsa izi, nthawi zambiri pochotsa limodzi la malingaliro osagwirizana. Mayiko otsuka masewera akuyembekeza kuti lingaliro lomwe lachotsedwa ndilokhudza ufulu wa anthu osati masewera
| sports | online news |
en11568 | This is where sportswashing becomes ethically problematic. To the degree that it distracts from wrongdoing, such as human rights violations, it can contribute to the perpetuation of that wrongdoing | Apa ndipamene kutsuka masewera kumakhala kovuta. Kufikira kumlingo umene umadodometsa kuchita zoipa, monga kuphwanya ufulu wachibadwidwe, ukhoza kuwonjezera kuchitika kwa zolakwazo
| sports | online news |
en11569 | Countries are often motivated to enact reforms when they experience pressure from other states, especially large democratic states that are reacting to internal public pressure. If the population is distracted by sport, then public pressure can wane | Mayiko nthawi zambiri amalimbikitsidwa kuti asinthe pamene akukakamizidwa ndi mayiko ena, makamaka mayiko akuluakulu a ufulu wa demokalase omwe akukhudzidwa ndi kukakamizidwa kwa anthu. Ngati anthu asokonezedwa ndi masewera, ndiye kuti kukakamizidwa ndi anthu kumatha kuchepa
| sports | online news |
en11570 | But just because someone was not aware of, or chose to ignore, the political dimension of the sporting event, that doesn’t mean they are absolved of responsibility. Sadly, sportswashing makes anyone involved in it complicit to some degree | Koma chifukwa chakuti wina samadziŵa, kapena anasankha kunyalanyaza, mbali ya ndale ya zochitika zamasewera, zimenezo sizikutanthauza kuti iwo achotsedwa udindo. Chomvetsa chisoni n'chakuti kutsuka masewera kumapangitsa kuti aliyense amene akukhudzidwa nawo achitepo kanthu
| sports | online news |
en11571 | There is an even greater ethical weight placed on the shoulders of sportspeople, who are often viewed as role models and whose behaviour can be seen to normalise certain values | Pali zolemetsa zokulirapo zomwe zimayikidwa pamapewa a anthu ochita masewera, omwe nthawi zambiri amawonedwa ngati zitsanzo komanso omwe khalidwe lawo limatha kuwoneka kuti limapangitsa kuti zinthu zizikhala bwino.
| sports | online news |
en11572 | This is why we place such emphasis on sportspeople behaving responsibly on and off the field, such as in nightclubs or in their private relationships | Ichi ndichifukwa chake timagomezera kwambiri kuti ochita masewerawa azichita zinthu moyenera mkati ndi kunja kwabwalo la masewera, monga m'malo osangalalira ausiku kapena maubwenzi awo amseri.
| sports | online news |
en11573 | If a sportsperson accepts money to participate in a sportswashed event, that sets a standard for others. And if they are aware of the ethically problematic nature of their hosts, then this opens them to a charge of hypocrisy | Ngati wosewera mpira avomereza ndalama kuti achite nawo masewera otsukidwawa, izi zimakhazikitsa muyezo kwa ena. Ndipo ngati akudziwa za zovuta za chikhalidwe cha omwe adawalandira, ndiye kuti izi zimawatsegulira mlandu wachinyengo. | sports | online news |
en11574 | However, there are ways of pushing back against sportswashing. The first is to refuse to support it financially, such as by not buying tickets to the events or subscriptions to the coverage in the media | Komabe, pali njira zochepetsera kutsutsana ndi kutsuka masewerawa. Choyamba ndikukana kuthandizira pachuma, monga kusagula matikiti opita kuzochitikazo kapena kulembetsa kwa wofalitsa nkhani.
| sports | online news |
en11575 | For some, this will mean missing out on watching a sacred sporting event, and it’s important not to understate how big a cost that might be for them | Kwa ena, izi zikutanthauza kuphonya kuwonera masewera opatulika, ndipo ndikofunikira kuti musachepetse kuti zikhoza kukhala zofunikira bwanji kwa iwo. | sports | online news |
en11576 | However, if they choose to watch, they can consider how to reduce or nullify the impact of the sportswashing. That could involve informing themselves and others about the true state of affairs, reducing the informational distortion caused by sportswashing | Komabe, ngati asankha kuwonera, angaganizire momwe angachepetsere kapena kuthetseratu vuto la kutsuka pamasewera. Izi zingaphatikizepo kudzidziwitsa iwo eni ndi ena za momwe zinthu zilili, kuchepetsa kufalizitsa kwabodza kwa chidziwitso komwe kumachitika chifukwa cha kutsuka masewera. | sports | online news |
en11577 | Sportspeople have an even greater responsibility but also a greater potential impact for good. Some have refused to participate in sportswashed events, such as golfer Tiger Woods, who reportedly turned down an offer in excess of $US 700 million to join the Saudi-backed LIV Tour | Osewera ali ndi udindo wokulirapo komanso zotsatira zake zabwino. Ena anakana kutenga nawo mbali pazamasewera, monga gofu Tiger Woods, yemwe akuti anakana mwayi wopitilira ndalama zokwana $ 700 miliyoni kuti alowe nawo ku mpikisano woyendetsedwa ndi Saudi. | sports | online news |
en11578 | When states are involved in funding sport, then sport can no longer be said to be removed from politics. Through sportswashing it becomes a political tool | Pamene mayiko akukhudzidwa ndi kupeleka ndalama zamasewera, ndiye kuti masewera sangathenso kuti achotsedwe mu ndale. Kupyolera mu kutsuka masewera kumakhala chida chandale | sports | online news |
en11579 | If we want to maintain sport as a pure and sacred pursuit, then we must consider how we choose to engage with it and how we might avoid or counteract the power of sportswashing to distract or normalize wrongdoing | Ngati tikufuna kusunga kuti masewera kukhala chinthu chopatulika komanso chopatulika, tiyenera kuganizira mmene timasankhira wochita nawo masewerawo ndi mmene tingapewere kapena kulimbana ndi mphamvu ya kutsuka maseŵera kuti tisokoneze kapena kusintha zoipa. | sports | online news |
en11580 | We are now five days into one of the most controversial World Cups in footballing history. The controversy lies not in the football that has been played but the way in which the tournament is being used by its host, Qatar, a country with a limited footballing pedigree and a troubling human rights record | Tsopano tili ndi masiku asanu mumpikisano wa World Cup womwe anthu ambiri sakugwirizana nawo m'mbiri ya mpira. Mkangano suli pa mpira womwe waseweredwa koma momwe mpikisanowu ukugwiritsidwira ntchito ndi Qatar, dziko lomwe lili ndi anthu ochepa okonda mpira komanso mbiri yozunza maufulu a anthu. | sports | online news |
en11581 | The starkness of this case makes it a useful context against which to explore the relationship between sportswashing and democracy | Kulimba kwa mlanduwu kumapangitsa kukhala kothandiza pofufuza ubale wapakati pamasewera ndi ufulu wa demokalase
| sports | online news |
en11582 | As a form of reputation laundering, sportswashing works to enhance the legitimacy of wrongdoers and shield them from the negative consequences of their conduct | Monga njira yochotsera zoipa, kutsuka maseŵera kumeteteza olakwawo kuti akhale ovomerezeka ndi kuwateteza ku zotsatirapo zoipa za khalidwe lawo.
| sports | online news |
en11583 | In so doing, it can embolden a sportswasher to commit further wrongdoings and help perpetuate weak governance | Potero, kungathe kulimbitsa mtima wosambitsa masewera kuti achite zolakwa zina ndikuthandizira kulimbikitsa ulamuliro wofooka.
| sports | online news |
en11584 | However, history suggests that such criticism tends to subside once the sport is underway - although at this early stage, it appears the World Cup in Qatar may buck this trend | Komabe, mbiri ikuwonetsa kuti kutsutsidwa kotereku kumachepa ngati masewerawa akupitilira - ngakhale pakali pano, zikuwoneka kuti World Cup ku Qatar ikhoza kuthana ndi izi.
| sports | online news |
en11585 | The immense size of the sports industry and the power of the individuals involved in sportswashing can leave the average fan feeling impotent | Kukula kwamakampani oyendetsa masewera komanso mphamvu za anthu omwe akuchita nawo masewera otsuka masewera amatha kusiya okonda masewerawa kudzimva kuti alibe mphamvu.
| sports | online news |
en11586 | However, scholars have recently argued that fan and athlete activism have an important role to play in resisting the phenomenon | Komabe, akatswiri anenapo posachedwapa kuti okonda masewerawa ndi wosewera ali ndi gawo lofunikira polimbana ndi zomwe zimachitika.
| sports | online news |
en11587 | When fans and athletes draw attention to abuses, particularly from within the emotionally charged atmosphere of a stadium, they undermine this separation and limit the event’s ability to distract | Pamene wotsatira masewerawa ndi othamanga akuwonetsa zoipa za zankhanza, makamaka zomwe zimachitika m'bwalo lamasewera, amalepheretsa kulekanitsidwa ndikuchepetsa kuthekera kwa chochitikacho kusokoneza.
| sports | online news |
en11588 | The Oct. 10 election has been widely seen as a test of support for former soccer star Weah, 57, who was criticized in his first term by the opposition and Liberia’s international partners for not doing enough to tackle corruption | Chisankho cha Oct. 10 chikuwoneka ngati mayeso chothandizira katswiri wakale wa mpira Weah, wazaka zakubanda makuni asanu asanu ndi ziwiri, yemwe adadzudzulidwa mu nthawi yake yoyamba ndi otsutsa komanso ogwirizana ndi mayiko a Liberia chifukwa chosagwira ntchito yokwanira kuthana ndi ziphuphu. | sports | online news |
en11589 | On his campaign trail, he asked voters for more time to fulfill his promise to rebuild the nation’s broken economy, institutions and infrastructure, pledging to pave more roads if reelected | Paulendo wake wochita kampeni, adapempha ovota nthawi yochulukirapo kuti akwaniritse lonjezo lake lokhonzanso chuma, mabungwe ndi zomangamanga, kulonjeza kuti adzakonza misewu yambiri ngati atasankhidwanso.
| sports | online news |
en11590 | The minister was responding to a question on whether government is committed to finalize construction of the stadia for the two domestic football powerhouses, having once again been left out in the proposed 2022/23 National Budget | Ndunayi imayankha funso loti ngati boma likufunitsitsa kumaliza ntchito yomanga mabwalo amasewera a magulu awiri amasewera ampira, atasiyidwanso mu ndondomeko ya cha chaka cha 2022/23.
| sports | online news |
en11591 | He said in an interview on Saturday: “The projects will be reviewed and the outcome will be made available to the public as well as Bullets and Wanderers | Iye adati poyankhulana Loweruka: “ntchitoyi aunikanso ndipo zotsatira zake zipelekedwa kwa anthu komanso Bullets ndi Wanderers.
| sports | online news |
en11592 | Building stadiums for Bullets and Wanderers was not on our agenda. Nevertheless, we will proceed with the projects. We have not abandoned them, but how we will do that is a subject for another day | Kumanga ma bwalo la masewero la Bullets ndi Wanderers sizinali pa m’ndanda wathu. Komabe, tipitiliza ndi ntchitoyi. Sitinawasiye, koma mmene tidzachitire zimenezo ndi nkhani ya tsiku lina
| sports | online news |
en11593 | He said: “Covid-19 and issues of the kwacha losing value means that the battle for resources to go to crucial social sectors will always overshadow the desire to fulfil political pledges made by any previous regime, not because they are not needed, but owing to resource challenges | Anatinso: “Covid-19 komanso kutsika kwa mphamvu kwa kwacha kukutanthauza kuti kulimbilana chuma kuti chipite kumagulu ofunikira nthawi zonse idzaphimba chikhumbo chokwaniritsa malonjezo a ndale omwe adalonjeza kale, osati chifukwa chosafunikira, koma chifukwa chakukumana ndi mavuto | sports | online news |
en11594 | Mind you, the past regime talked about building a new stadium in Blantyre and designs of the infrastructure were produced, including the Kwacha Park location yet funds were not set aside for that | Tangoganizani, boma lidakambapo zomanga bwalo latsopano ku Blantyre ndipo zidapangidwa, kuphatikiza malo wochezelapo a Kwacha koma ndalama sizinapelekedwe kuti zitheke.
| sports | online news |
en11595 | In addition, the Bullets and Wanderers projects, pledged by the past regime, hardly took off before a change of government happened. In other words, it was more of a political gimmick prior to elections than something serious | Kuonjezera apo, ntchito za bwalo la masewera la Bullets ndi Wanderers, omwe lidalonjeza boma lapitalo, siinayambe ngakhale pomwe boma lisanasinthe. Mwa kuyankhula kwina, zinali zandale zandale osati kuti zikhoza kuchitikadi
| sports | online news |
en11596 | In December, Bullets unveiled plans to construct their own 20 000-capacity stadium in Mpemba, Blantyre along Chikwawa Road as part of their ambitious project to build the club’s village | Mu December, Bullets idatukutsa ndondomeko yomanga bwalo lawo lamasewera lokwana anthu 20 000 ku Mpemba, Blantyre m’mbali mwa msewu wa Chikwawa ngati imodzi mwantchito zawo zomanga mudzi wa timuyi.
| sports | online news |
en11597 | The 13 hectares space, situated about seven kilometres outside Blantyre Central Business District, will also include office complex, two training pitches, hostels, club house and a conference centre | Dera la mahekitala khumi ndi atatu, lomwe lili pamtunda wa makilomita asanu ndi ziwiri kuchokera ku malo Blantyre Central Business District, liphatikizanso maofesi, mabwalo awiri ophunzirira, malo ogona, malo osangalira ndi malo ochitira misonkhano.
| sports | online news |
en11598 | On why they were planning to construct a stadium when government already pledged to build one for them whose preliminary phase was already done, the People’s Team vice-president Fleetwood Haiya then said: “We are aware of government’s pledge but to avoid being caught off guard, we have thought it wise to build our own | Pazifukwa zomwe akhonzekera kumanga bwalo pomwe boma lidalonjeza kale kuti liwamangira lomwe gawo lake loyamba lidachitika kale, wachiwiri kwa mtsogoleri wa timu yokonda anthuyi Fleetwood Haiya adati: , tawona kuti n’chanzeru kumanga chanthu | sports | online news |
en11599 | The use of sport to promote peace and development is not entirely new; the Olympics are a historic example of sport used for a higher purpose | Kugwiritsa ntchito masewera pofuna kulimbikitsa mtendere ndi chitukuko sichachilendo; Masewera a Olimpiki ndi chitsanzo chamasewera omwe amagwiritsidwa ntchito pazinthu zapamwamba | sports | online news |
en11600 | However, until recently, sport has remained on the sidelines of mainstream humanitarian and development programming, considered a luxury in the context of other development objectives |
Komabe, kufikira posachedwapa, masewera akhalabe pambali pa ntchito zothandizira anthu ndi chitukuko, zomwe zimaoneka ngati zongosalatsa chabe pofananiza ndi zachitukuko zina.
| sports | online news |
en11601 | Now, though, there is a growing understanding that sport does not have to compete with other priorities but can | Tsopano, komabe, pali kumvetsetsa kokulirapo kwakuti maseŵera sakuyenera kupikisana ndi zinthu zina zofunika koma angathe
| sports | online news |
en11602 | actually be a means for addressing them | kukhala njira yothanirana nawo
| sports | online news |